[00:54.11] CHICHEWA [00:56.95] Siyani dumbo [00:58.70] Siyani umbombo [01:00.58] Tatopa nazo kodi simukudziwa kuti lija ndi kale? [01:06.86] Siya umbanda [01:11.38] Siya zauchigawenga [01:14.04] Kodi watani iwe siukudziwa kuti kupha ndi sambi? [01:21.28] Siyani dumbo [01:24.02] Hear me now [01:27.65] Hear me now [01:30.36] Hear me now [01:33.91] Hear me now [01:40.25] Hear me now [01:45.65] Hear me now [02:17.23] Siya kaduka [02:19.99] Siya zokonda kuba [02:23.64] Siyani chinyengo kuyambila lero tiyeni tikonze tsogolo [02:30.89] Siyani kugona [02:34.42] Siya kugona tulo [02:37.15] Kunja kwacha kodi simukuona kuti dzuwa latuluka? [02:44.38] Siya kaduka [02:47.05] Hear me now [02:49.73] Hear me now [02:53.43] Hear me now [02:57.08] Hear me now [03:04.25] Hear me now [03:07.85] Hear me now [03:15.07] Dzaka makumi asanu [03:45.72] Zatha kufika lero [03:49.41] Mpaka lero umphawi [03:52.11] Ukungophabe dziko [03:54.84] Dzaka makumi asanu [03:58.46] Zatha kufika lero [04:02.02] Mpaka lero umphawi [04:05.62] Ukungophabe dziko [04:36.33]